Yesu Adza Kuwerenga

 


Yesu adza kuwerenga
Ana ake abwino,
Ndi kubvala zachifumu
Zakuwalazo zake.


Chorus
Ana ake angonga
Nyenyezi zam’mwamba,
Adzawala m’Ufumu
Wa Mbuye Yesu.


Yesu adza kukundika
Ana ake ankhosa,
Ndiye Mbusa wakufatsa
Namalezatu lere.


Kudzachera tsiku lijalo
Msangatu msanga,
Kudzawala m’mawa wake
Pompano ponse.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *